Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 May tsamba 15
  • June 28–July 4

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • June 28–July 4
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 May tsamba 15

June 28–July 4

DEUTERONOMO 9-10

  • Nyimbo Na. 49 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi Yehova Mulungu Wanu Akufuna Kuti Muzichita Chiyani?”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • De 9:1-3​—Ngakhale kuti ana a Anaki anali “amphamvu ndi aatali,” n’chifukwa chiyani Aisiraeli sankafunika kuwaopa? (it-1 103)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) De 10:1-22 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 3)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti, N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo? ndipo kenako kambiranani naye mfundo za muvidiyoyi. (th phunziro 9)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) fg phunziro 12 ¶4-5 (th phunziro 18)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 135

  • Kodi Mumakonda Kusewera Magemu a Pakompyuta?: (7 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani omvera mafunso otsatirawa: Kodi magemu a pakompyuta angakhale ndi mavuto otani? Kodi ndi zinthu ziti zomwe n’zofunika kwambiri kuposa magemu a pakompyuta? (Aef 5:15, 16) Kodi magemu amene mumakonda kusewera amasonyeza kuti ndinu munthu wotani? Kodi mungatani kuti magemu a pakompyuta asamakulamulireni?

  • “Muzisankha Zinthu Mwanzeru pa Nkhani ya Mowa”: (8 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti, Ganizirani Zimene Zingachitike Ngati Mutamwa Mowa.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs Kalata Yochokera ku Bungwe Lolamulira, mutu 1 ndime 1-6, Mawu Akumapeto 1

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 105 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena