Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 November tsamba 5
  • November 15-21

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • November 15-21
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 November tsamba 5

November 15-21

YOSWA 23-24

  • Nyimbo Na. 50 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Mawu Omaliza Amene Yoswa Analimbikitsa Nawo Mtundu wa Aisiraeli”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Yos 24:2​—Kodi Tera yemwe anali bambo ake a Abulahamu ankalambira mafano? (w04 12/1 12 ¶1)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Yos 24:19-33 (th phunziro 11)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 2)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako mugawireni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 20)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lffi phunziro 01 zomwe taphunzira, kubwereza, komanso zolinga (th phunziro 3)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 28

  • Muzipewa Kugwirizana ndi Anthu a Makhalidwe Oipa Kuntchito: (7 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muzipewa Zinthu Zimene Zingawononge Khalidwe Lanu la Kukhulupirika​—Kugwirizana ndi Anthu a Makhalidwe Oipa. Kenako funsani mafunso otsatirawa: Kodi kuchita zinthu ndi anthu a makhalidwe oipa kuntchito kunakhudza bwanji mlongoyu? Kodi anasintha chiyani, nanga zinamuthandiza bwanji? Kodi vidiyoyi yakuphunzitsani chiyani pankhani yopewa kugwirizana ndi anthu a makhalidwe oipa?

  • Mukhoza Kupeza Mabwenzi Kulikonse: (8 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani mafunso otsatirawa: Kodi ndi mavuto ati amene anachititsa kuti Akil ayambe kugwirizana ndi anyamata a makhalidwe oipa kusukulu? Kodi anapeza bwanji anzake abwino mumpingo? Kodi vidiyoyi yakuphunzitsani chiyani pa nkhani yopeza anzanu abwino?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 7 ndime 20-28, mfundo za m’Baibulo tsa. 100-103

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 67 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena