November 22-28
OWERUZA 1-3
Nyimbo Na. 126 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Nkhani ya Kulimba Mtima Komanso Yochititsa Chidwi”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Owe 2:10-12—Kodi nkhani imeneyi ikutichenjeza chiyani ifeyo? (w05 1/15 24 ¶7)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Owe 3:12-31 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
“Zimene Mungachite Kuti Muzisangalala Kwambiri mu Utumiki—Muzilola Kuti Yehova Azikuthandizani Kudzera M’pemphero”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muzigwiritsa Ntchito Zomwe Yehova Watipatsa Kuti Muzisangalala ndi Ntchito Yophunzitsa—Pemphero.
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lffi phunziro 02 mawu oyamba komanso mfundo 1-3 (th phunziro 11)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Khalani Bwenzi la Yehova—Uzichita Zinthu Bwino mu Utumiki: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako ngati n’kotheka, pemphani ana amene munawasankhiratu kuti abwere kupulatifomu ndipo afunseni mafunso awa: Kodi tingakonzekere bwanji utumiki? Kodi tingatani kuti tizioneka bwino komanso tizivala mwaulemu? Kodi tingatani kuti tizisonyeza makhalidwe abwino mu utumiki?
“Mfundo Zothandiza Kuti Msonkhano Wokonzekera Utumiki Uzikhala Wabwino”: (10 min.) Nkhani yokambirana yokambidwa ndi woyang’anira utumiki. Funsani omvera kuti afotokoze ubwino wofika pa msonkhano wokonzekera utumiki mwamsanga.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 8 ndime 1-7
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 31 ndi Pemphero