Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 November tsamba 8
  • November 29–December 5, 2021

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • November 29–December 5, 2021
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 November tsamba 8

November 29–December 5

OWERUZA 4-5

  • Nyimbo Na. 137 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yehova Anagwiritsa Ntchito Akazi Awiri Populumutsa Anthu Ake”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Owe 5:20​—Kodi nyenyezi zinamenya nkhondo motani kuchokera kumwamba pothandiza Baraki? (w05 1/15 25 ¶5)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Owe 4:1-16 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Kenako mugawireni Nsanja ya Olonda Na. 2 2021. (th phunziro 1)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako mugawireni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 4)

  • Nkhani: (5 min.) w06 3/1 28-29​—Mutu: Kodi ‘akazi ayenera kukhala chete m’mipingo’ m’njira iti?​—1Ak 14:34. (th phunziro 14)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 84

  • “Kodi Alongo Angatani Kuti Azichita Zambiri Potumikira Yehova?”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti “Akazi Ogwira Ntchito Mwakhama Potumikira Ambuye”.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 8 ndime 8-18, mawu akumapeto 22

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 149 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena