Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 November tsamba 12
  • December 13-19

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • December 13-19
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 November tsamba 12

December 13-19

OWERUZA 8-9

  • Nyimbo Na. 125 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kudzichepetsa N’kwabwino Osati Kunyada”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Owe 8:27​—Kodi Gidiyoni ankalambira efodi yemwe anapanga? (it-1 753 ¶1)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Owe 8:28–9:6 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Wobwereza: (3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza (th phunziro 9)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, ndipo yambitsani phunziro la Baibulo. (th phunziro 20)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lffi phunziro 02 mfundo 4 (th phunziro 13)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 108

  • Zimene Gulu Lathu Lachita: (5 min.) Onerani vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya December.

  • Zofunika Pampingo: (10 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 9 ndime 1-8, mawu akumapeto 23, 24

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 38 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena