Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 January tsamba 3
  • January 10-16

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • January 10-16
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 January tsamba 3

January 10-16

OWERUZA 17-19

  • Nyimbo Na. 88 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kusamvera Malamulo a Mulungu Kumabweretsa Mavuto”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Owe 19:18​—N’chifukwa chiyani dzina lakuti Yehova linaikidwa pa lembali mu Baibulo la Dziko Latsopano la Chingelezi lokonzedwanso mu 2013? (w15 12/15 10 ¶6)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Owe 17:1-13 (th phunziro 2)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Ulendo Wobwereza: Mulungu Amatisamalira​—Yer 29:11. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.

  • Ulendo Wobwereza: (3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza. (th phunziro 6)

  • Ulendo Wobwereza: (5 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako mugawireni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, ndipo yambitsani phunziro la Baibulo pogwiritsa ntchito phunziro 01. (th phunziro 13)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 89

  • Khalani Bwenzi la Yehova​—Muzimvera Makolo Anu: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako ngati n’zotheka, funsani ana omwe munawasankhiratu mafunso awa: Kodi Kalebe anasonyeza bwanji kuti sanamvere mayi ake? Nanga anakonza bwanji zimene analakwitsa? N’chifukwa chiyani muyenera kumvera makolo anu?

  • Zofunika Pampingo: (5 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 10 ndime 13-18, mawu akumapeto 25

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 131 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena