Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 January tsamba 14
  • February 21-27

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • February 21-27
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 January tsamba 14

February 21-27

1 SAMUELI 6-8

  • Nyimbo Na. 9 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi Mfumu Yanu ndi Ndani?”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 1Sa 7:3​—Kodi lembali likutiphunzitsa chiyani pa nkhani ya kutembenuka ndi kulapa? (w02 4/1 12 ¶13)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Sa 7:1-14 (th phunziro 2)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Gawirani magazini yomwe ili ndi nkhani imene mwininyumba watchula. (th phunziro 12)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Muitanireni kumisonkhano yathu. (th phunziro 18)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lffi phunziro 03 zomwe taphunzira, kubwereza komanso zolinga (th phunziro 20)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 28

  • Zofunika Pampingo: (10 min.)

  • Kodi Mudzachita Upainiya Wothandiza M’mwezi wa March Kapena April?: (5 min.) Nkhani yokambirana, yochokera mu nkhani yomwe ili mu Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu ka January-February 2021, tsamba 16.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 12 ndime 9-14, mawu akumapeto 27

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 29 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena