Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 March tsamba 4
  • March 21-27

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • March 21-27
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 March tsamba 4

March 21-27

1 SAMUELI 16-17

  • Nyimbo Na. 7 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yehova Ndiye Mwini Nkhondo”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 1Sa 16:14, mawu a m’munsi​—Kodi Sauli analandira “mzimu woipa wochokera kwa Yehova” m’njira yotani? (it-2 871-872)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Sa 16:1-13 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Kuitanira Anthu ku Chikumbutso: (2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene poitanira anthu ku Chikumbutso. (th phunziro 11)

  • Kuitanira Anthu ku Chikumbutso: (3 min.) Itanirani mnzanu wakuntchito, wakusukulu kapena wachibale wanu amene munamulalikirapo m’mbuyomu. (th phunziro 2)

  • Ulendo Wobwereza: (3 min.) Pangani ulendo wobwereza kwa munthu amene anasonyeza chidwi ndipo analandira kapepala komuitanira ku Chikumbutso. (th phunziro 4)

  • Ulendo Wobwereza: (3 min.) Pangani ulendo wobwereza kwa munthu amene anasonyeza chidwi ndipo analandira kapepala komuitanira ku Chikumbutso. Mudziwitseni za webusaiti yathu. (th phunziro 20)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 150

  • “Njira Zitatu Zimene Zingatithandize Kuti Tizidalira Yehova”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Palibe Chifukwa Choti Tiziopa Kuzunzidwa.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 13 ndime 23-26, mfundo za m’Baibulo tsa. 184-186

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 9 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena