Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 March tsamba 12
  • April 18-24

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • April 18-24
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 March tsamba 12

April 18-24

1 SAMUELI 23-24

  • Nyimbo Na. 114 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Tiziyembekezera Yehova Moleza Mtima”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 1Sa 23:16, 17​—Kodi tingatsanzire bwanji chitsanzo cha Yonatani? (w17.11 27 ¶11)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Sa 23:24–24:7 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zimene anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo (th phunziro 6)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. M’patseni chimodzi mwa Zinthu Zophunzira. (th phunziro 13)

  • Nkhani: (5 min.) w19.03 23-24 ¶12-15​—Mutu: Muzileza Mtima ndi Amene Mukuphunzira Nawo. (th phunziro 14)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 128

  • “Mavuto Onse Ali Ndi Tsiku Lothera”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Anthu Ogwirizana M’dziko Limene Anthu ake Sagwirizana.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 14 ndime 18-19, mfundo za m’Baibulo tsa. 196-199

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 29 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena