Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 March tsamba 14
  • April 25–May 1

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • April 25–May 1
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 March tsamba 14

April 25–May 1

1 SAMUELI 25-26

  • Nyimbo Na. 130 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi Mumachita Zinthu Mopupuluma?”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 1Sa 25:18, 19​—N’chifukwa chiyani sitinganene kuti Abigayeli sankagonjera mwamuna wake monga mutu wa banja? (ia 80 ¶16)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Sa 25:1-13 (th phunziro 2)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • “Zimene Mungachite Kuti Muzisangalala Kwambiri mu Utumiki​—Muzithandiza Ophunzira Anu Kuti Akhale pa Ubwenzi ndi Yehova”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muzithandiza Amene Mukuphunzira Nawo Baibulo Kuti Akhale pa Ubwenzi ndi Yehova.

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 04 mfundo 4 (th phunziro 9)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 126

  • Zofunika Pampingo: (15 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 01

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 98 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena