Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 May tsamba 12
  • June 20-26

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • June 20-26
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 May tsamba 12

June 20-26

2 SAMUELI 13-14

  • Nyimbo Na. 127 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kudzikonda kwa Aminoni Kunabweretsa Mavuto”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 2Sa 14:25, 26​—Kodi chitsanzo cha Abisalomu chimatiphunzitsa chiyani pa nkhani ya kukongola? (g05 1/8 24-25)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Sa 14:8-20 (th phunziro 2)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Gawirani magazini yomwe ili ndi nkhani imene mwininyumba anatchula. (th phunziro 12)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Muitanireni kumisonkhano yathu. (th phunziro 18)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 05 mfundo 6 komanso Zimene Ena Amanena (th phunziro 18)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 68

  • “Muzigwiritsa Ntchito Buku Lakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale Polimbitsa Chikhulupiriro Chanu mwa Yehova Ndi Yesu”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muzilimbitsa Chikhulupiriro Chanu mwa Yehova Pogwiritsa Ntchito Buku Lakuti “Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale” komanso yakuti Muzilimbitsa Chikhulupiriro Chanu mwa Yesu Pogwiritsa Ntchito Buku Lakuti “Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale.”

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 09

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 47 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena