Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 May tsamba 15
  • “Chikondi . . . Sichidzikuza”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Chikondi . . . Sichidzikuza”
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • “Pitirizani Kusonyeza Chikondi”
    Yandikirani Yehova
  • Chikondi (Agape)—Zimene Sichili ndi ZImene Chili
    Nsanja ya Olonda—1993
  • Kulani M’chikondi
    Nsanja ya Olonda—2001
  • Njira ya Chikondi Silephera
    Nsanja ya Olonda—1999
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 May tsamba 15
Zithunzi: 1. M’bale akupemphera asanayambe kuwerenga Baibulo. 2. M’bale yemwe uja akukolopa ku Nyumba ya Ufumu. 3. M’bale uja ndi mkazi wake akukaona mlongo wachikulire kuchipatala.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

“Chikondi . . . Sichidzikuza”

Chikondi chimatithandiza kuti tizisonyeza kuti ndife odzichepetsa. (1Ak 13:4) Tikamakonda abale athu, sitimadziona kukhala ofunika kwambiri kuposa iwowo. Timaona zabwino mwa anthu ena ndipo timagwiritsa ntchito maluso athu powathandiza. (Afi 2:3, 4) Tikamakonda kwambiri abale athu, ndi pamene Yehova angamatigwiritse ntchito pochita chifuniro chake.

ONERANI VIDIYO YAKUTI MUZIKUMBUKIRA ZIMENE CHIKONDI CHIMACHITA KOMANSO ZIMENE SICHICHITA​—SICHIDZIKUZA, KENAKO YANKHANI MAFUNSO OTSATIRAWA:

  • Kodi Abisalomu anali ndi mphatso ziti?

  • Kodi anagwiritsa ntchito bwanji molakwika mphatso zakezi?

  • Kodi tingatani kuti tipewe kudzikuza?​—Aga 5:26

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena