Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 July tsamba 2
  • July 4-10

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • July 4-10
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 July tsamba 2

July 4-10

2 SAMUELI 18-19

  • Nyimbo Na. 138 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Barizilai Anali Wodzichepetsa”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 2Sa 19:24-30​—Kodi chitsanzo cha Mefiboseti chingatithandize bwanji? (w20.04 30 ¶19)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Sa 19:31-43 (th phunziro 2)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Ulendo Woyamba: Cholinga cha Mulungu​—Ge 1:28. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba.a Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 1)

  • Nkhani: (5 min.) w21.08 23-25 ¶15-19​—Mutu: Kodi ndi Zolinga Ziti Zimene Tingakhale Nazo Ngati Zinthu pa Moyo Wathu Sizikutilola Kuchita Zambiri? (th phunziro 20)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 81

  • “Mukhale ndi Zolinga mu Chaka Chautumiki Chikubwerachi​—Upainiya”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muzichita Zinthu Molimba Mtima​—Apainiya.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 11

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 97 ndi Pemphero

a Onani nkhani imene ili pa tsamba 16.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena