Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 July tsamba 4
  • July 11-17

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • July 11-17
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 July tsamba 4

July 11-17

2 SAMUELI 20-21

  • Nyimbo Na. 62 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yehova ndi Mulungu Wachilungamo”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 2Sa 21:15-17​—Kodi tikuphunzira chiyani pa nkhaniyi? w13 1/15 31 ¶14)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Sa 20:1-13 (th phunziro 2)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Ulendo Wobwereza: Cholinga cha Mulungu​—Yes 55:11. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.

  • Ulendo Wobwereza: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mufotokozereni kuti timaphunzira Baibulo ndi anthu ndipo m’patseni khadi lodziwitsa anthu za phunziro la Baibulo. (th phunziro 4)

  • Ulendo Wobwereza: (5 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. M’patseni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale ndipo musonyezeni mmene phunziro la Baibulo limachitikira. (th phunziro 11)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 58

  • “Mukhale ndi Zolinga mu Chaka Chautumiki Chikubwerachi​—Samukirani Kumene Kukufunika Olalikira Ufumu Ambiri”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Lowani pa Khomo la Utumiki Mwachikhulupiriro​—Samukirani Kumene Kukufunika Olalikira Ufumu Ambiri.

  • “Mmene Tingagwiritsire Ntchito Zitsanzo za Zimene Tinganene”: (5 min.) Nkhani yokambidwa ndi Woyang’anira Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 12

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 3 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena