Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 July tsamba 8
  • August 1-7

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • August 1-7
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 July tsamba 8

August 1-7

1 MAFUMU 1-2

  • Nyimbo Na. 98 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi Mumaphunzirapo Kanthu Mukalakwitsa Zinazake?”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 1Mf 2:37, 41-46​—Kodi tingaphunzire chiyani pa zimene Simeyi analakwitsa? (w05 7/1 30 ¶2)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Mf 1:28-40 (th phunziro 2)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Mugawireni khadi lodziwitsa anthu za jw.org. (th phunziro 11)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Kodi pa Nyumba ya Ufumu Pamachitika Zotani? ndipo muitanireni ku misonkhano yathu. (th phunziro 20)

  • Nkhani: (5 min.) km 1/15 2 ¶1-3​—Mutu: Muziphunzira Kuchokera kwa Anthu Amene Amalalikira Mogwira Mtima. (th phunziro 13)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 84

  • “Mukhale ndi Zolinga mu Chaka Chautumiki Chikubwerachi​—Funsirani Sukulu ya Akhristu Olalikira za Ufumu”: (7 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Lowani pa Khomo la Utumiki Mwachikhulupiriro​—Funsirani Sukulu ya Akhristu Olalikira za Ufumu.

  • “Mukhale ndi Zolinga mu Chaka Chautumiki Chikubwerachi​—Thandizani pa Ntchito Yazomangamanga”: (8 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Lowani pa Khomo la Utumiki Mwachikhulupiriro​—Thandizani pa Ntchito Yazomangamanga.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 14

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 24 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena