August 8-14
1 MAFUMU 3-4
Nyimbo Na. 88 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Nzeru Ndi Zamtengo Wapatali”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
1Mf 4:20—Kodi mawu akuti “ngati mchenga wa m’mphepete mwa nyanja” amatanthauza chiyani? (w98 2/1 11 ¶15)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Mf 3:1-14 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Mufotokozereni kuti timaphunzira Baibulo ndi anthu ndipo m’patseni khadi lodziwitsa anthu za phunziro la Baibulo. (th phunziro 1)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako m’patseni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale ndipo yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti, Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji? (th phunziro 3)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 06 mfundo 4 (th phunziro 12)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (10 min.)
Mukhale ndi Zolinga mu Chaka Chautumiki Chikubwerachi—Muzikhala Opatsa: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Lowani pa Khomo la Utumiki Mwachikhulupiriro—‘Muziika Kenakake Pambali’ Kothandizira pa Ntchito ya Yehova. Kenako yankhani funso lotsatirali: Kodi banjali linasonyeza bwanji kuti linali lopatsa?
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 15 ndi mawu akumapeto 2
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 14 ndi Pemphero