Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 September tsamba 4
  • September 12-18

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • September 12-18
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 September tsamba 4

September 12-18

1 MAFUMU 11-12

  • Nyimbo Na. 137 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Sankhani Mwanzeru Munthu Wokwatirana Naye”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 1Mf 12:21-24​—Kodi tikuphunzira chiyani kwa Mfumu Rehobowamu pa nkhani ya kumvera? (w18.06 14 ¶1-4)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Mf 12:21-33 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene pa ntchito yapadera yoyambitsa maphunziro a Baibulo. (th phunziro 3)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Pitirizani phunziro la Baibulo lomwe munayambitsa pa ulendo woyamba, pogwiritsa ntchito phunziro 01 la kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 11)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 07 mfundo 4 (th phunziro 8)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 132

  • “Banja Ndi Mgwirizano wa Moyo Wonse”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Kukonzekera Kulowa M’banja​—Gawo 3: “Kuwerengera Ndalama Zimene Mudzawononge.”

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 19 mfundo 1-4

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 63 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena