Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 September tsamba 12
  • October 24-30

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • October 24-30
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 September tsamba 12

October 24-30

2 MAFUMU 1-2

  • Nyimbo Na. 79 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Chitsanzo Chabwino cha Kuphunzitsa Ena”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 2Mf 2:11​—Kodi Eliya anapita kuti atatengedwa “mumphepo yamkuntho n’kukwera kumwamba”? (w05 8/1 9 ¶1)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mf 2:1-10 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 12)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mufotokozereni kuti timaphunzira Baibulo ndi anthu ndipo m’patseni khadi lodziwitsa anthu za phunziro la Baibulo. (th phunziro 13)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 07 zomwe taphunzira, kubwereza komanso zolinga (th phunziro 14)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 53

  • “Zinthu Zothandiza Zomwe Zili M’buku Lakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Funsani mwachidule wofalitsa mmodzi amene akuchititsa phunziro la Baibulo pogwiritsa ntchito buku la Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale: Kodi n’chiyani chimakusangalatsani mukamagwiritsa ntchito bukuli? Kodi mavidiyo komanso mafunso akuthandiza bwanji wophunzira wanu?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 24

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 66 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena