Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 September tsamba 14
  • October 31–November 6

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • October 31–November 6
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 September tsamba 14

October 31–November 6

2 MAFUMU 3-4

  • Nyimbo Na. 151 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Nyamulani Mwana Wanu”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 2Mf 4:38​—Kodi n’kutheka kuti “ana a aneneri” anali ndani? (it-2 697 ¶2)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mf 3:1-12 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 17)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji? (th phunziro 20)

  • Nkhani: (5 min.) w13 8/15 28-29​—Mutu: Kodi Mungatsanzire Bwanji Elisa pa Nkhani ya Kudzichepetsa Mukamachita Utumiki Wopatulika? (th phunziro 15)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 129

  • “Kufikira Pamene Adzakhalenso Ndi Moyo”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Zimene Mungachite Mukaferedwa.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 25

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 139 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena