Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 November tsamba 10
  • December 12-18

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • December 12-18
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 November tsamba 10

December 12-18

2 MAFUMU 16-17

  • Nyimbo Na. 115 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kuleza Mtima kwa Yehova Kuli ndi Malire”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 2Mf 17:29​—Kodi “Asamariya” otchulidwa pa lembali anali ndani, nanga dzinali linkaimira ndani patapita nthawi? (it-2 847)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mf 17:18-28 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene muli chitsanzo cha ulendo woyamba. Mufotokozereni za webusaiti yathu ya jw.org, ndipo mugawireni khadi lodziwitsa anthu za webusaitiyi. (th phunziro 4)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene muli chitsanzo cha ulendo wobwereza. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo? kenako kambiranani naye mfundo za muvidiyoyi. (th phunziro 20)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 08 mfundo 5 (th phunziro 9)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 3

  • “Muziyembekezera Mapeto a Dzikoli Molimba Mtima”: (5 min.) Nkhani yokambirana.

  • Zimene Gulu Lathu Lachita: (10 min.) Onerani vidiyo yakuti Zimene Gulu Lathu Lachita ya December.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 31

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 74 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena