January 30–February 5
1 MBIRI 7-9
Nyimbo Na. 84 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yehova Angakuthandizeni Kuti Mukwanitse Kuchita Utumiki Wovuta”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
1Mb 9:33—Kodi vesili likutithandiza bwanji kumvetsa kuti nyimbo ndi zofunika kwambiri pa kulambira koona? (w10 12/15 21 ¶6)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Mb 7:1-13 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Mugawireni khadi lodziwitsa anthu za jw.org. (th phunziro 16)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 20)
Nkhani: (5 min.) w21.06 3-4 ¶3-8—Mutu: Muzithandiza Wophunzira Baibulo Kuti Azigwiritsa Ntchito Zimene Akuphunzira. (th phunziro 13)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Yehova Amatithandiza Tikamakumana ndi Mayesero”: (15 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 36
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 31 ndi Pemphero