Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 May tsamba 6
  • May 15-21

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • May 15-21
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 May tsamba 6

May 15-21

2 MBIRI 22-24

  • Nyimbo Na. 73 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yehova Amadalitsa Anthu Amene Amachita Zinthu Molimba Mtima”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 2Mb 24:22​—Kodi zimene Zekariya ananena mu ulosi wa palembali zinakwaniritsidwa bwanji? (it-2 1223 ¶13)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mb 22:1-12 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 1)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Muitanireni kumisonkhano yathu. (th phunziro 17)

  • Nkhani: (5 min.) w10 2/15 6-8 ¶6-10​—Mutu: Mzimu wa Yehova Udzakuthandizani Kukhala Olimba Mtima. (th phunziro 8)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 55

  • Zofunika Pampingo: (15 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 45 mfundo 4, zomwe taphunzira, kubwereza komanso zolinga

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 37 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena