Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 May tsamba 8
  • May 29–June 4

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • May 29–June 4
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 May tsamba 8

May 29–June 4

2 MBIRI 28-29

  • Nyimbo Na. 54 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Mukhoza Kutumikira Yehova Ngakhale Makolo Anu Si Chitsanzo Chabwino”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 2Mb 29:25​—Kodi chitsanzo cha Natani chikutiphunzitsa chiyani pankhani ya ubwino wotsatira uphungu wochokera kwa Yehova? (w12 2/15 24-25)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mb 28:1-11 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 4)

  • Ulendo Wobwereza: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 19)

  • Phunziro la Baibulo: (6 min.) lff phunziro 10 mfundo 4 (th phunziro 13)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 56

  • “Yehova ndi ‘Tate wa Ana Amasiye’”: (8 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo.

  • Zofunika Pampingo: (7 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 47

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 86 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena