Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 July tsamba 5
  • July 17-23

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • July 17-23
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 July tsamba 5

July 17-23

EZARA 9-10

  • Nyimbo Na. 89 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kusamvera Kumapweteketsa”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Eza 10:44​—N’chifukwa chiyani akazi ndi ana awo anawatumiza kwawo? (w06 1/15 20 ¶2)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Eza 9:1-9 (th phunziro 2)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito kapepala kakuti Kodi Mavuto Amene Tikukumana Nawowa Adzathadi? kuti muyambe kukambirana nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 13)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Muitanireni ku misonkhano yathu, ndipo yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Kodi pa Nyumba ya Ufumu Pamachitika Zotani? kenako kambiranani naye mfundo za muvidiyoyi. (th phunziro 6)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 11 mawu oyamba komanso mfundo 1-3 (th phunziro 14)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 150

  • Kumvera Kumatiteteza (2At 1:8): (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani mafunso otsatirawa: Kodi n’chiyani chichitike Aramagedo isanachitike?

    Kodi kukhala omvera kumatithandiza bwanji panopa?

    Kodi pali kugwirizana kotani pakati pa Aramagedo ndi kumvera?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 50 mfundo 6-7, zomwe taphunzira, kubwereza komanso zolinga

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 133 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena