Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 July tsamba 6
  • July 24-30

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • July 24-30
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 July tsamba 6

July 24-30

NEHEMIYA 1-2

  • Nyimbo Na. 47 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Nthawi Yomweyo Ndinapemphera”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Ne 2:4​—Kodi aka kanali koyamba kuti Nehemiya apemphere zokhudza nkhaniyi, nanga tikuphunzirapo chiyani? (w86 2/15 25)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Ne 2:11-20 (th phunziro 2)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Kenako mufotokozereni za webusaiti yathu ya jw.org, ndipo mugawireni khadi lodziwitsa anthu za webusaitiyi. (th phunziro 16)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 3)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 11 mawu oyamba pa mbali yakuti Fufuzani Mozama komanso mfundo 4 (th phunziro 11)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 44

  • Khalani Bwenzi la Yehova​—Kodi Yehova Amayankha Mapemphero?: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani omvera kuti, Kodi vidiyoyi ikutiphunzitsa chiyani zokhudza pemphero?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 51

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 102 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena