Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 July tsamba 8
  • August 7-13

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • August 7-13
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 July tsamba 8

August 7-13

NEHEMIYA 5-7

  • Nyimbo Na. 17 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Nehemiya Ankafuna Kutumikira, Osati Kutumikiridwa”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Ne 6:13​—N’chifukwa chiyani likanakhala tchimo Nehemiya akanati akabisale m’kachisi? (w07 7/1 30 ¶15)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Ne 5:1-13 (th phunziro 2)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo? kenako kambiranani naye mfundo za muvidiyoyi. (th phunziro 9)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 6)

  • Nkhani: (5 min.) w13 5/15 7 ¶17-19​—Mutu: Alaliki Abwino Amathandizana. (th phunziro 20)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 90

  • “Amachita Khama Kuti Atitumikire”: (15 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 53

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 35 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena