Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 July tsamba 12
  • August 21-27

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • August 21-27
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 July tsamba 12

August 21-27

NEHEMIYA 10-11

  • Nyimbo Na. 37 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Anasiya Zinthu Zina Chifukwa cha Yehova”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Ne 10:34​—N’chifukwa chiyani anthu ankafunika kupititsa nkhuni ku nyumba ya Mulungu? (w06 2/1 11 ¶1)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Ne 10:28-39 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Muitanireni ku misonkhano yathu ndipo yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Kodi pa Nyumba ya Ufumu Pamachitika Zotani? (th phunziro 1)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako mugawireni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, ndipo kambiranani naye mwachidule kamutu kakuti “Zimene Mungachite Kuti Muzipindula ndi Phunziro Lililonse.” (th phunziro 4)

  • Nkhani: (5 min.) w11 2/15 15-16 ¶12-15​—Mutu: Nsembe Zimene Mulungu Amavomereza Masiku Ano. (th phunziro 20)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 81

  • “Kodi Muli ndi Zolinga Zotani M’chaka Chautumiki Chikubwerachi?”: (10 min.) Nkhani yokambirana.

  • “Ntchito Yapadera Yolengeza za Ufumu wa Mulungu mu September”: (5 min.) Nkhani yokambidwa ndi woyang’anira utumiki. Limbikitsani anthu kuti adzagwire ntchitoyi mwakhama, ndipo fotokozani zimene mpingo wanu wakonza.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 55 mfundo 1-4

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 92 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena