Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 July tsamba 14
  • August 28–September 3

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • August 28–September 3
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 July tsamba 14

August 28–September 3

NEHEMIYA 12-13

  • Nyimbo Na. 34 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Muzikhala Okhulupirika kwa Yehova Mukamasankha Anthu Ocheza Nawo”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Ne 13:10​—Oimba a pakachisi anali Alevi, ndiye n’chifukwa chiyani anatchulidwa mosiyana? (it-2 452 ¶9)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Ne 12:27-39 (th phunziro 2)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Mufotokozereni za webusaiti yathu ya jw.org, ndipo mugawireni khadi lodziwitsa anthu za webusaitiyi. (th phunziro 16)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mufotokozereni kuti timaphunzira Baibulo ndi anthu, ndipo mugawireni khadi lodziwitsa anthu za phunziro la Baibulo. (th phunziro 3)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 11 zomwe taphunzira, kubwereza komanso zolinga (th phunziro 20)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 108

  • Zofunika Pampingo: (5 min.)

  • “Tsanzirani Chikondi Chokhulupirika cha Yehova”: (10 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 55 mfundo 5, zomwe taphunzira, kubwereza komanso zolinga

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 84 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena