Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 September tsamba 9
  • October 9-15

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • October 9-15
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 September tsamba 9

October 9-15

YOBU 4-5

  • Nyimbo Na. 121 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Samalani ndi Nkhani Zabodza”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Yob 4:4—Kodi Yobu anapereka chitsanzo chabwino chiti kwa Akhristu masiku ano? (w03 5/15 22 ¶5-6)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Yob 5:​1-27 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 min.) Gwiritsani ntchito nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 4)

  • Ulendo Wobwereza: (5 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Musonyezeni mmene angapezere zinthu zosiyanasiyana pa jw.org. (th phunziro 15)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 16 mfundo 5 (th phunziro 16)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 78

  • Zofunika Pampingo: (15 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 60

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 38 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena