Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 September tsamba 12
  • October 23-29

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • October 23-29
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 September tsamba 12

October 23-29

YOBU 8-10

  • Nyimbo Na. 107 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Chikondi Chokhulupirika cha Mulungu Chimatiteteza ku Mabodza a Satana”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Yob 9:32—Kodi tizitani ngati tawerenga nkhani inayake m’Baibulo imene sitikuimvetsa? (w10 10/15 6-7 ¶19-20)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Yob 9:​20-35 (th phunziro 11)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 17)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni kabuku ka Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, ndipo kambiranani naye mwachidule mfundo zimene zili pa mutu wakuti “Zimene Mungachite Kuti Muzipindula ndi Phunziro Lililonse.” (th phunziro 3)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 16 mfundo 6 komanso Zimene Ena Amanena (th phunziro 14)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 109

  • “Muzithandiza Anthu Osapembedza Kudziwa Mlengi Wawo”: (10 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo.

  • Zofunika Pampingo: (5 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) bt “Kalata Yochokera ku Bungwe Lolamulira” komanso mutu 1 ¶1-7

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 64 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena