Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 November tsamba 10
  • December 11-17

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • December 11-17
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 November tsamba 10

December 11-17

YOBU 25-27

  • Nyimbo Na. 34 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Sitifunika Kukhala Angwiro Kuti Tikhale Okhulupirika”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Yob 26:14—Kodi zinthu zochepa zokhudza chilengedwe zomwe timadziwa zimatithandiza kumvetsa chiyani zokhudza Yehova? (w16.11 9 ¶3)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Yob 25:1–26:14 (th phunziro 12)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 min.) Gwiritsani ntchito nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 1)

  • Ulendo Wobwereza: (5 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Musonyezeni mmene angapezere nkhani yomwe yamusangalatsa pa jw.org. (th phunziro 17)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 13 mawu oyamba komanso mfundo 1-3 (th phunziro 15)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 45

  • “Kukhulupirika Kumagwirizana ndi Zimene Timaganiza”: (5 min.) Nkhani yokambirana.

  • Zimene Gulu Lathu Lachita: (10 min.) Onerani vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya December.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) bt mutu 3 ¶4-11

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 57 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena