December 25-31
YOBU 30-31
Nyimbo Na. 28 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Zimene Yobu Anachita Kuti Akhalebe Woyera”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Yob 31:35—Kodi tingatani kuti tisakhale ngati anzake a Yobu munthu wina akamatifotokozera mavuto ake? (w05 11/15 11 ¶3)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Yob 31:15-40 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Mufotokozereni kuti timaphunzira Baibulo ndi anthu ndipo m’patseni khadi lodziwitsa anthu za phunziro la Baibulo. (th phunziro 1)
Ulendo Wobwereza: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Muitanireni kumisonkhano yathu ndipo yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Kodi pa Nyumba ya Ufumu Pamachitika Zotani?, kenako kambiranani naye mfundo za muvidiyoyi? (th phunziro 11)
Nkhani: (5 min.) g16.4 8-9—Mutu: Kodi Ndingafotokoze Bwanji Zimene Baibulo Limanena pa Nkhani ya Kugonana kwa Amuna Kapena Akazi Okhaokha? (th phunziro 14)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“N’chifukwa Chiyani Kuonera Zolaula N’koipa?”: (7 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo.
Zofunika Pampingo: (8 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) bt mutu 4 ¶1-8
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 74 ndi Pemphero