Nkhani Zimene Zatuluka Pa Jw Library Komanso Jw.Org
BAIBULO LIMASINTHA ANTHU
Moyo Wanga Unkangoipiraipirabe
Solomone anasamukira ku United States pofuna kukhala ndi moyo wabwino. Koma m’malomwake, anayamba kugwiritsa ntchito mankhwala osokoneza bongo ndipo anamangidwa. N’chiyani chinamuthandiza kuti asinthe moyo wake?
Pa JW Library, pitani pamene alemba kuti PUBLICATIONS > ARTICLE SERIES > THE BIBLE CHANGES LIVES.
Pa jw.org, pitani pamene alemba kuti ZOKHUDZA IFEYO > ZOCHITIKA PA MOYO WA A MBONI ZA YEHOVA > BAIBULO LIMASINTHA ANTHU.
ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA
Ndingatani Ngati Anzanga Amandiona Kuti Ndine Wotsalira?
Kodi kukondedwa ndi anthu omwe makhalidwe awo si abwino n’kofunika kusiyana ndi kutsatira mfundo zimene mukudziwa kuti ndi zabwino?
Pa JW Library, pitani pamene alemba kuti PUBLICATIONS > ARTICLE SERIES > YOUNG PEOPLE ASK.
Pa jw.org, pitani pamene alemba kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACHINYAMATA > ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA.