Nkhani Zimene Zatuluka Pa Jw Library Komanso Jw.Org
ZOCHITIKA PA MOYO WA A MBONI ZA YEHOVA
“Ndimachita Zomwe Ndingakwanitse”
Ngakhale kuti ali ndi zaka pafupifupi 90, a Irma amalemba makalata ofotokoza mfundo za m’Baibulo ndipo anthu ambiri amakhudzidwa mtima kwambiri akalandira makalatawa.
Pa JW Library, pitani pamene alemba kuti PUBLICATIONS > ARTICLE SERIES > EXPERIENCES.
Pa jw.org, pitani pamene alemba kuti ZOKHUDZA IFEYO > ZOCHITIKA PA MOYO WA A MBONI ZA YEHOVA > KUUZA ENA CHOONADI CHA M’BAIBULO.
ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA
Ndingatani Kuti Ndizikonda Masewera Olimbitsa Thupi?
Kuwonjezera pa kukhala ndi thanzi labwino, kodi masewera olimbitsa thupi angakuthandizeninso bwanji?
Pa JW Library, pitani pamene alemba kuti PUBLICATIONS > ARTICLE SERIES > YOUNG PEOPLE ASK.
Pa jw.org, pitani pamene alemba kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACHINYAMATA > ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA.