Magazini Yophunzira
AUGUST 2021
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: SEPTEMBER 27–OCTOBER 31, 2021
© 2021 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
CHITHUNZI CHAPACHIKUTO:
Banja likulalikira kumene kukufunika olalikira ambiri, mlongo wachitsikana akuthandiza pantchito yomanga Nyumba ya Ufumu, banja lachikulire likulalikira pa telefoni. Onsewa akusangalala ndi zimene akuchita pa utumiki wawo (Onani nkhani yophunzira 34, ndime 11)