Magazini Yophunzira
OCTOBER 2021
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: DECEMBER 6, 2021–JANUARY 2, 2022
© 2021 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
CHITHUNZI CHAPACHIKUTO:
Ngakhale kuti Nowa analalikira mokhulupirika kwa zaka zambiri, palibe amene analowa m’chingalawa kupatulapo iye ndi anthu a m’banja lake. Ngakhale zinali choncho, Nowa ankamverabe Mulungu. (Onani nkhani yophunzira 43, ndime 11)