Magazini Yophunzira
NOVEMBER 2021
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: JANUARY 3-30, 2022
© 2021 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
CHITHUNZI CHAPACHIKUTO:
Rute sakufuna kusiyana ndi apongozi ake a Naomi, pamene Olipa akubwerera ku Mowabu. Rute akuuza Naomi kuti: “Kumene inu mupite inenso ndipita komweko” (Onani nkhani yophunzira 45, ndime 13)