Nkhani Zimene Zatuluka Pa JW Library Komanso JW.ORG
NKHANI ZINA
Baibulo limasonyeza chimene chimachititsa kuti anthu azichita zauchigawenga komanso mmene Mulungu amamvera ndi zimenezi. Baibulo limafotokozanso lonjezo la Mulungu lodzathetsa mantha ndi zachiwawa.
ZOCHITIKA PA MOYO WA A MBONI ZA YEHOVA
A Mboni za Yehova Anayankha Modekha Atakumana ndi Ansembe Olusa
Baibulo limatilimbikitsa kuti tizikhala odekha ngakhale pamene ena atiputa. Kodi malangizo amenewa ndi othandiza?
KODI ZOPEREKA ZANU ZIMAGWIRITSIDWA NTCHITO BWANJI?
Ntchito Yomanga Inayenda Bwino Mliri Usanayambe
Tinakonza zoti timange kapena kukonzanso malo olambirira oposa 2,700 m’chaka cha utumiki cha 2020. Ndiye kodi mliri wa COVID-19 unakhudza bwanji zomwe tinakonzazi?