Magazini Yophunzira
JUNE 2023
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: AUGUST 14–SEPTEMBER 10, 2023
© 2023 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
CHITHUNZI CHAPACHIKUTO:
Gidiyoni anamvera Yehova ndipo anachepetsa chiwerengero cha asilikali ake posankha amuna 300 omwe anasonyeza kuti ndi atcheru (Onani nkhani yophunzira 25, ndime 9)