Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w23 November tsamba 1-32
  • Magazini Yophunzira

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Magazini Yophunzira
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2023
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2023
w23 November tsamba 1-32
Ezara ndi Aisiraeli ena ali pakachisi, akulira. Sekaniya akuthandiza Ezara kuti aimirire.

Magazini Yophunzira

NOVEMBER 2023

NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: JANUARY 8–FEBRUARY 4, 2024

© 2023 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.

Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.

CHITHUNZI CHAPACHIKUTO:

Ezara ali kukachisi ndipo akulira komanso kupemphera chifukwa cha machimo a anthu. Gulu nalonso likulira. Kenako Sekaniya akulimbikitsa Ezara pomuuza kuti: “Aisiraeli ali ndi chiyembekezo . . . ndipo ife tili nawe.”—Ezara 10:​2, 4 (Onani nkhani yophunzira 48, ndime 17)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena