Magazini Yophunzira
JANUARY 2024
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: MARCH 4–APRIL 7, 2024
© 2023 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
LEMBA LA CHAKA CHA 2024:
“Ndikamachita mantha, ndimadalira inu.”—SAL. 56:3.
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.