B12-A
Wiki Yomaliza ya Moyo wa Yesu Padziko Lapansi (Gawo 1)
Yerusalemu ndi Madera Ozungulira
Kachisi
Munda wa Getsemane (?)
Nyumba ya Bwanamkubwa
Nyumba ya Kayafa (?)
Nyumba imene Herode Antipa ankakhala (?)
Damu la Betizata
Dziwe la Siloamu
Holo ya Khoti Lalikulu la Ayuda (?)
Gologota (?)
Munda Wamagazi (?)
Sankhani tsiku: Nisani 8 | Nisani 9 | Nisani 10 | Nisani 11
Nisani 8 (Sabata)
MADZULO (Masiku a Ayuda amayamba ndi kutha dzuwa litalowa)
Anafika ku Betaniya kutatsala masiku 6 kuti Pasika achitike
M’MAWA
MADZULO
Nisani 9
MADZULO
Anakadya kunyumba ya Simoni wakhate
Mariya anadzoza Yesu mafuta a nado
Ayuda anabwera kudzaona Yesu ndi Lazaro
M’MAWA
Analowa mu Yerusalemu ndipo anthu anasangalala
Anaphunzitsa m’kachisi
MADZULO
Nisani 10
MADZULO
Anakhala usiku wonse ku Betaniya
M’MAWA
Analawirira kupita ku Yerusalemu
Anathamangitsa ogulitsa malonda m’kachisi
Yehova analankhula kuchokera kumwamba
MADZULO
Nisani 11
MADZULO
M’MAWA
Anaphunzitsa m’kachisi pogwiritsa ntchito mafanizo
Anadzudzula Afarisi mwamphamvu
Anaona mkazi wamasiye akuponya timakobidi tiwiri
Paphiri la Maolivi, ananeneratu za kuwonongedwa kwa Yerusalemu ndi chizindikiro cha kukhalapo kwake