3 YOHANE ZIMENE ZILI MʼBUKULI Moni komanso pemphero (1-4) Anayamikira Gayo (5-8) Diotirefe wodzikuza (9, 10) Demetiriyo anamuchitira umboni kuti ankachita zabwino (11, 12) Kukonza zoti akawachezere; kuwapatsa moni (13, 14)