CHIVUMBULUTSO
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
Chivumbulutso chochokera kwa Mulungu, kudzera mwa Yesu (1-3)
Moni wopita kumipingo 7 (4-8)
Atadzazidwa ndi mzimu woyera, Yohane anapezeka kuti ali mʼtsiku la Ambuye (9-11)
Masomphenya a Yesu, atalandira ulemerero (12-20)
2
3
4
5
Mpukutu umene anaumata ndi zidindo 7 (1-5)
Mwanawankhosa anatenga mpukutuwo (6-8)
Mwanawankhosa ndi woyenera kumatula zidindozo (9-14)
6
7
Angelo 4 anagwira mphepo kuti zisawononge (1-3)
Anthu okwana 144,000 anaikidwa chidindo (4-8)
Khamu lalikulu limene lavala mikanjo yoyera (9-17)
8
Anamatula chidindo cha 7 (1-6)
Kuliza malipenga 4 oyambirira (7-12)
Analengeza zokhudza masoka atatu (13)
9
10
11
12
Mkazi, mwana wamwamuna ndi chinjoka (1-6)
Mikayeli anamenyana ndi chinjoka (7-12)
Chinjoka chinazunza mkazi (13-17)
13
Chilombo cha mitu 7 chinatuluka mʼnyanja (1-10)
Chilombo cha nyanga ziwiri chinatuluka pansi (11-13)
Chifaniziro cha chilombo cha mitu 7 (14, 15)
Chizindikiro komanso nambala ya chilombo (16-18)
14
Mwanawankhosa ndi enanso 144,000 (1-5)
Mauthenga ochokera kwa angelo atatu (6-12)
Osangalala ndi anthu amene akufa ali ogwirizana ndi Khritsu (13)
Anakolola mpesa kawiri padziko lapansi (14-20)
15
16
17
18
Kugwa kwa “Babulo Wamkulu” (1-8)
Kulirira Babulo amene wagwa (9-19)
Kumwamba kudzakhala chisangalalo chifukwa cha kugwa kwa Babulo (20)
Babulo adzaponyedwa mʼnyanja ngati mwala (21-24)
19
Tamandani Ya chifukwa cha ziweruzo zake (1-10)
Amene anakwera pahatchi yoyera (11-16)
Phwando lalikulu la Mulungu la chakudya chamadzulo (17, 18)
Chilombo chinagonjetsedwa (19-21)
20
Satana adzamangidwa kwa zaka 1,000 (1-3)
Amene adzalamulire ndi Khristu kwa zaka 1,000 (4-6)
Satana adzamasulidwa, kenako adzawonongedwa (7-10)
Akufa adzaweruzidwa pamaso pa mpando wachifumu woyera (11-15)
21
22