Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g00 11/8 tsamba 1-2
  • Zamkatimu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zamkatimu
  • Galamukani!—2000
  • Nkhani Yofanana
  • Ntchito Yofunika ya Anamwino
    Galamukani!—2000
  • Anamwino—Kodi N’chifukwa Chiyani Ali Ofunikira kwa Ife?
    Galamukani!—2000
  • ‘Anatiphunzitsa Kulemekeza Chipembedzo Chake’
    Nsanja ya Olonda—2004
  • Kodi Nyenyezi Zolosera za M’tsogolo Ziyenera Kulamulira Moyo Wanu?
    Galamukani!—2000
Onani Zambiri
Galamukani!—2000
g00 11/8 tsamba 1-2

Zamkatimu

November 8, 2000

Thanzi Labwino—Kodi Pali Zosankha Zotani?

Kufunika kwa chithandizo chamankhwala ogwiritsidwa ntchito masiku onse ndiponso kwa chithandizo chamankhwala osagwiritsidwa ntchito masiku onse n’kodziŵika bwino kwambiri lerolino. Kodi zina mwa njira zochiritsira zomwe zimatchedwa kuti chithandizo chamankhwala chosagwiritsidwa ntchito masiku onse ndi ziti? Ndipo n’chifukwa chiyani anthu ambiri akuzigwiritsa ntchito?

3 Thanzi Labwino—Kodi Lingapezeke Mwanjira Zochiritsira Zatsopano?

4 Njira Zochiritsira Zosagwiritsidwa Ntchito Masiku Onse—Chifukwa Chomwe Anthu Ambiri Amazigwiritsira Ntchito

6 Kupenda Njira Zochiritsira Zosagwiritsidwa Ntchito Masiku Onse

11 Chosankha Chanu pa Chithandizo Chamankhwala

13 Achinyamata Akufunsa Kuti . . .

Kodi Ndiyenera Kufotokozera Munthu Wina Kuti Ndikuvutika Maganizo?

18 Anawapulumutsa Lokumbakumba

19 Anamwino—Kodi N’chifukwa Chiyani Ali Ofunikira kwa Ife?

21 Ntchito Yofunika ya Anamwino

31 Kufuna Kuchotsa Boma la Vatican M’bungwe la UN

Kodi Nyenyezi Zolosera za M’tsogolo Ziyenera Kulamulira Moyo Wanu? 16

Anthu miyandamiyanda amapenda nyenyezi kuti apeze malangizo. Kodi kuopsa kwake n’kotani?

Kuyesedwa kwa Chikhulupiriro ku Poland 28

Kodi n’chifukwa chiyani munthu ameneyu anazunzidwa ndi kuikidwa m’ndende mobwerezabwereza m’kati mwa zaka makumi ambiri pambuyo pa nkhondo yachiŵiri yapadziko lonse?

[Mawu a Chithunzi patsamba 2]

Anatomy Improved and Illustrated, London, 1723, Bernardino Genga

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena