Zamkatimu
August 8, 2001
Kuletsa Udani Kuti Usapitirire
Udani ukupitirizabe kubweretsa mantha ndiponso mikangano yobutsa chiwawa. Kodi udaniwu unachokera kuti? Kodi ndi wotheka kuwugonjetsa?
3 Udani Wasanduka Mliri Wapadziko Lonse
8 Kuletsa Udani Kuti Usapitirire
12 Matenda Opatsirana Amaopsa Koma Amapeŵeka
13 Anthu Othandiza Ali Kwina Kulikonse
16 Anthu Ongodzipereka Akugwiradi Ntchito
20 Ntchito Yongodzipereka Yokhala ndi Mapindu Okhalitsa
32 Si la Achinyamata Ang’onoang’ono Okha
Marabou—Mbalame Imene Amailakwira 26
Anthu ena amati mbalame ya Marabou n’njankhanza ndiponso n’njonyansa. Komabe mbalameyi ili ndi zinthu zingapo zochititsa chidwi
Kuyambira kalekale kwambiri anthu akhala akusemphana maganizo pankhani yakuti wokana Kristu ndani. Kodi umboni umene ulipo umasonyeza zotani?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
AP Photo/John Gillis