Zamkatimu
October 8, 2002
Mabanja Akholo Limodzi Angayende Bwinobwino
Mabanja akholo limodzi ayamba kuchuluka m’mayiko ambiri. Kodi mavuto awo angathetsedwe bwanji?
3 Mabanja Akholo Limodzi Akuchuluka Kwambiri
6 Makolo Olera Ana Ali Okha Amakhala ndi Mavuto Ambiri
10 Kholo Lopanda Linzake Koma Losasoŵa Wolithandiza
25 Zida Zopha Mwachinsinsi—Kodi Zingasakazedi Anthu?
30 Kufunafuna Njira Zothetsera Vutoli
32 N’zotheka Kukhala ndi Banja Losangalala!
Kodi Zinthu Zakale Zofukulidwa Pansi N’zofunikadi Kuti Tikhale ndi Chikhulupiriro? 16
Kodi kuti tikhale ndi chikhulupiriro chakuti Baibulo ndi Mawu a Mulungu tiyenera kudziŵa kaye zimene akatswiri apeza pofukula zinthu zakale?
Kodi Anthu Okonda Zinthu Zonyamula Mtima Amakopekeranji ndi Maseŵera Angozi? 18
Anthu ochuluka kwabasi akumachita nawo maseŵera angozi. Kodi n’chifukwa chiyani iwo akutero?