Zamkatimu
June 8, 2003
Kodi Anthu Asinthiranji Masiku Ano?
Anthu padzikoli akusintha moipa kwambiri. Kodi kusintha kumeneku kumakukhudzani motani?
4 Kodi Anthu Akusiya Kutsatira Mfundo Zabwino?
7 Kodi Mumaona Kuti Chinachake Chikusoŵeka Chifukwa Choti Anthu Asintha?
10 Boma Lodzalimbikitsa Mfundo za Mulungu
19 Matenda Ofalitsidwa Ndi Tizilombo Akuvutitsa Kwambiri
22 N’chifukwa Chiyani Ayambiranso?
30 Kodi Ndingatani ndi Mavuto Oleredwa ndi Makolo Osandibereka?
Kodi Baibulo limati tiziyankhula motani kwa ena?
M’nkhalango ya Nairobi Zinyama Zimangodziyendera 15
M’nkhalango ya Nairobi National Park, zinyama zimakhala moyandikana ndi anthu.