Zamkatimu
December 8, 2003
Kodi Misonkho Yanu ndi Yokwera Kwambiri?
Padziko lonse lapansi, nthaŵi zambiri anthu amadana ndi kukhoma misonkho. N’chifukwa chiyani malamulo a zamisonkho ndi ovuta kumvetsa, ndipo n’chifukwa chiyani misonkho ndi yokwera kwambiri? Kodi muyenera kukhoma misonkho?
3 Kodi Kudana ndi Misonkho Kukuwonjezeka?
5 Kodi Timakhoma Misonkho Kuti Tikhale ndi “Chitukuko”?
10 Kodi Muyenera Kukhoma Misonkho?
12 Achinyamata Akufunsa Kuti . . .
Kodi Ndingatani Kuti Anthu Asamangofanizira Zochita Zanga ndi za Mbale Wanga?
15 Sopo ndi “Katemera Amene Mungadzipatse Nokha”
16 Anthu Amatengera Mmene Mlengi Analengera Zinthu
17 Chakudya Chochokera M’dimba Lanu
19 Kodi Dziko Lathu Lapansili Likudwala Kwambiri Motani?
20 Kodi Zatiyendera Bwanji Pankhani Yoteteza Chilengedwe?
25 Mmene Dziko Lapansili Lidzapulu Mutsidwire
32 Zisonyezero za Voliyumu 84 ya Galamukani!
Kodi muyenera kuda nkhaŵa motani mwana wanu akatentha thupi? Kodi mungathandize bwanji mwana wanu kuti apeze bwino?
[Chithunzi patsamba 2]
Anthu osagwirizana ndi kukhoma misonkho akulimbana ndi apolisi
[Mawu a Chithunzi]
AFP/Getty Images