Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g04 10/8 tsamba 1-2
  • Zamkatimu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zamkatimu
  • Galamukani!—2004
  • Nkhani Yofanana
  • Vuto Lapadziko Lonse la Atsikana Otenga Mimba Ali Aang’ono
    Galamukani!—2004
  • Kusanduka Azimayi Akadali Ana
    Galamukani!—2004
  • Kuthandiza ndi Kuteteza Atsikana
    Galamukani!—2004
  • Zamkatimu
    Galamukani!—2002
Onani Zambiri
Galamukani!—2004
g04 10/8 tsamba 1-2

Zamkatimu

October 8, 2004

Vuto Lapadziko Lonse la Atsikana Otenga Mimba Ali Aang’ono

Atsikana ambiri amakhala ndi vuto lolera okha ana. Kodi zingatheke kuti zinthu ziwayendere bwino? Kodi njira yabwino kwambiri yothandizira atsikana kuti apeŵe vuto limeneli ndi yotani?

3 Kusanduka Azimayi Akadali Ana

4 Vuto Lapadziko Lonse la Atsikana Otenga Mimba Ali Aang’ono

8 Kulimbana ndi Mavuto Amene Amakhalapo Munthu Akakhala Mayi Akadali Wamng’ono

11 Kuthandiza ndi Kuteteza Atsikana

13 Yehova, Mwandipeza!”

18 Sukulu Yamkaka Yopanda Zoseŵeretsa

19 Ana Ambiri Akubadwa Kudzera M’njira Zothandizira Anthu Osabereka Kuti Abereke

22 Njira Zatsopanozi Zabweretsanso Mavuto Atsopano

22 Matenda Osintha Mtundu wa Khungu

32 Izi N’zomwe Achinyamata Amafunikira

Kodi Anthu Okalamba Tiyenera Kuwachitira Zinthu Motani? 16

Malipoti akusonyeza kuti m’mayiko ambiri, anthu okalamba akunyalanyazidwa ndi kuchitiridwa nkhanza. Kodi Baibulo limaphunzitsa kuti okalamba tiziwaona bwanji?

Kodi Kumwa Moŵa Wambiri Nthaŵi Imodzi Kuli ndi Vuto Lanji? 29

Kodi kumwa moŵa wambiri nthaŵi imodzi n’kutani? Kodi kuopsa komwa moŵa mwauchidakwa n’kotani, makamaka kwa achinyamata?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena